Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 31:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kodi Efraimu ndiye mwana wanga wokondedwa? Kodi ndiye mwana wokondweretsa? nthawi zonse zoti ndimnenera zomtsutsa, pakuti ndimkumbukiranso ndithu; cifukwa cace mumtima mwanga ndimlirira; ndidzamcitiradi cifundo, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 31

Onani Yeremiya 31:20 nkhani