Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 3:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Kwezera maso ako ku mapiri oti se, nuone: sanagona ndi iwe kuti? Panjira wakhalira iwo, monga M-arabu m'cipululu; ndipo waipitsa dziko ndi zigololo zako, ndi zoipa zako.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:2 nkhani