Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 3:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Amati, Ngati mwamuna acotsa mkazi wace, ndipo amcokera iye, nakhala mkazi wa wina, kodi adzabweranso kwa mkaziyo? dzikolo kodi silidzaipitsidwa? Koma iwe wacita dama ndi mabwenzi ambiri; koma bweranso kwa Ine, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:1 nkhani