Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 3:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pa nthawi yomweyo adzacha Yerusalemu mpando wa Yehova; ndipo mitundu yonse idzasonkhanidwa kumeneko, ku dzina la Yehova, ku Yerusalemu; ndipo sadzayendanso konse m'kuumirira kwa mtima wao woipa.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 3

Onani Yeremiya 3:17 nkhani