Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 29:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, kuti, Cifukwa watumiza akalata m'dzina lako iwe mwini kwa anthu onse amene akhala ku Yerusalemu, ndi kwa Zefaniya mwana wace wa Maseya wansembe, ndi kwa ansembe onse, kuti.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:25 nkhani