Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 29:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo am'nsinga onse a Yuda amene ali m'Babulo adzatemberera pali iwo, kuti, Yehova akucitire iwe monga Zedekiya ndi Ahabu, amene mfumu ya ku Babulo inaoca m'moto;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:22 nkhani