Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 29:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli, za Ahabu mwana wace wa Koliya, ndi za Zedekiya mwana wace wa Maseya, amene anenera zonama m'dzina langa: Taonani, Ndidzawapereka m'dzanja la Nebukadirezara mfumu ya ku Babulo; ndipo Iye adzawapha pamaso panu;

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 29

Onani Yeremiya 29:21 nkhani