Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 28:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Ndaika gori lacitsulo pa khosi la amitundu onsewa, kuti amtumikire Nebukadinezara mfumu ya ku Babulo; ndipo adzamtumikira iye; ndipo ndampatsanso nyama za kuthengo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 28

Onani Yeremiya 28:14 nkhani