Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 28:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yeremiya mneneri ananena kwa Hananiya mneneri, Tamvatu, Hananiya; Yehova sanakutuma iwe; koma ukhulupiritsa anthu awa zonama.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 28

Onani Yeremiya 28:15 nkhani