Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 25:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo uziti kwa iwo, Atero Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli: Imwani inu, ndi kuledzera, ndi kusanza, ndi kugwa, osanyamukanso konse, cifukwa ca lupanga limene ndidzatumiza mwa inu.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 25

Onani Yeremiya 25:27 nkhani