Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 23:33 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene anthu awa, kapena mneneri, kapena wansembe, adzakufunsa iwe, kuti, Katundu wa Yehova ndi ciani? pamenepo uziti kwa iwo, Katundu wanji? Ndidzakucotsani inu, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 23

Onani Yeremiya 23:33 nkhani