Ndipo Pasuri mwana wace wa Imeri wansembe, amene anali kapitao wamkuru m'nyumba ya Yehova, anamva Yeremiya alikunenera zimenezi.