Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 19:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nuti, Tamvani mau a Yehova, inu mafumu a Yuda, ndi okhala m'Yerusalemu; Yehova wa makamu, Mulungu wa Israyeli atero, Taonani, ndidzatengera malo ano coipa, cimene ali yense adzacimva, makutu ace adzacita woo.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 19

Onani Yeremiya 19:3 nkhani