Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 16:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti Yehova atero, Usalowe m'nyumba ya maliro, usanke kukacita maliro ao, kapena kuwalirira; pakuti ndacotsa mtendere wanga pa anthu awa, cifundo ndi nsoni zokoma, ati Yehova.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16

Onani Yeremiya 16:5 nkhani