Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 16:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Adzafa ndi imfa zanthenda; sadzaliridwa maliro, sadzaikidwa; adzakhala ngati ndowe panthaka; ndipo adzathedwa lupanga, ndi njala; ndipo mitembo yao idzakhala cakudya ca mbalame za kumlengalenga, ndi zirombo za dziko lapansi.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 16

Onani Yeremiya 16:4 nkhani