Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 13:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti monga mpango uthina m'cuuno ca munthu, comweco ndinathinitsa kwa Ine nyumba yonse ya Israyeli ndi nyumba yonse ya Yuda, ati Yehova, kuti akhale kwa Ine anthu, ndi dzina, ndi cilemekezo, ndi ulemerero; koma anakana kumva.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 13

Onani Yeremiya 13:11 nkhani