Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 12:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala kuti nditazula iwo, ndidzabwera, ndipo ndidzawacitira cisoni; ndipo ndidzabwezanso iwo, yense ku colowa cace, ndi yense ku dziko lace.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 12

Onani Yeremiya 12:15 nkhani