Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 12:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo padzakhala kuti, ngati iwo adzaphunzira mwakhama njira za anthu anga, kulumbira ndi dzina langa, Pali Yehova; monga anaphunzitsa anthu anga kulumbira pali Baala; pamenepo ndidzamangitsa mudzi wao pakati pa anthu anga.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 12

Onani Yeremiya 12:16 nkhani