Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Yeremiya 12:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Yehova ponenera anansi anga onse oipa, amene akhudza colowa cimene ndalowetsamo anthu anga Israyeli; taonani, ndidzazula iwo m'dziko lao, ndipo ndidzazula nyumba ya Yuda pakati pao.

Werengani mutu wathunthu Yeremiya 12

Onani Yeremiya 12:14 nkhani