Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Oweruza 14:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo amuna a pamudzi anati kwa Samsoni tsiku lacisanu ndi ciwiri, lisanalowe dzuwa, Cozuna coposa uci nciani; ndi camphamvu coposa mkango nciani? Pamenepo ananena nao,Mukadapanda kulima ndimthandi wanga,Simukadakumika mwambi wanga.

Werengani mutu wathunthu Oweruza 14

Onani Oweruza 14:18 nkhani