Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Obadiya 1:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo andende a khamu ili la ana a Israyeli, okhala mwa Akanani, adzakhala naco colowa cao mpaka pa Zarefati; ndi andende a ku Yerusalemu okhala m'Sefaradi adzakhala nayo midzi ya kumwela, colowa cao.

Werengani mutu wathunthu Obadiya 1

Onani Obadiya 1:20 nkhani