Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Obadiya 1:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo akumwela adzakhala nalo phiri la Esau colowa cao; ndi iwo a kucidikha adzakhala nalo dziko la Afilisti; ndipo adzakhala nayo minda ya Efraimu, ndi minda ya Samariya colowa cao; ndi Benjamini adzakhala nalo la Gileadi.

Werengani mutu wathunthu Obadiya 1

Onani Obadiya 1:19 nkhani