Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Obadiya 1:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nyumba ya Yakobo idzakhala moto, ndi nyumba ya Yosefe lawi, ndi nyumba ya Esau ngati ciputu, ndipo adzawatentha pakati pao, ndi kuwapsereza; ndipo sadzakhalapo otsalira nyumba ya Esau; pakuti Yehova wanena.

Werengani mutu wathunthu Obadiya 1

Onani Obadiya 1:18 nkhani