Ha, mapazi ako akongola m'zikwakwata,Mwana wamkaziwe wa mfumu!Pozinga m'cuuno mwako pakunga zonyezimira,Nchito ya manja a mmisiri waluso.