Milomo yako ikunga mbota yofiira,M'kamwa mwako ndi kukoma:Palitsipa pako pakunga phande la khangazaPatseri pa cophimba cako.