Khosi lako likunga nsanja ya Davide anaimangira zida,Apacikapo zikopa zikwi,Ngakhale zikopa zonse za amuna amphamvu,