Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 9:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ngakhale masiku awiri, kapena mwezi, kapena masiku ambiri, pokhalitsa mtambo pamwamba pa kacisi ndi kukhalapo, ana a Israyeli anakhala m'cigono, osayenda ulendo; koma pakukwera uwu, anayenda ulendo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 9

Onani Numeri 9:22 nkhani