Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 9:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mtambo ukakhala kuyambira madzulo kufikira m'mawa; pokwera mtambo m'mawa, ayenda ulendo; ngakhale msana ngakhale usiku, pokwera mtambo, ayenda ulendo.

Werengani mutu wathunthu Numeri 9

Onani Numeri 9:21 nkhani