Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 8:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Alevi anadziyeretsa, natsuka zobvala zao; ndi Aroni anawapereka ngati nsembe yoweyula pamaso pa Yehova; ndi Aroni anawacitira cotetezera kuwayeretsa.

Werengani mutu wathunthu Numeri 8

Onani Numeri 8:21 nkhani