Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:36 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamene Balaki anamva kuti wafika Balamu, anamturukira kukakomana naye ku mudzi wa Moabu, wokhala m'mphepete mwa Arinoni, ndiwo ku malekezero a malire ace.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:36 nkhani