Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 22:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo buru anati kwa Balamu, Si ndine buru wako amene umayenda wokwera pa ine ciyambire ndiri wako kufikira lero lino? Kodi ndikakucitira cotere ndi kale lonse? Ndipo anati, Iai.

Werengani mutu wathunthu Numeri 22

Onani Numeri 22:30 nkhani