Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:39 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Eleazara wansembe anatenga mbale zofukiza zamkuwa, zimene anthu opsererawo adabwera nazo; ndipo anazisula zaphanthiphanthi zikhale cibvundikilo ca guwala nsembe;

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:39 nkhani