Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 16:40 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cikhale cikumbutso kwa ana a Israyeli, kuti mlendo, wosati wa mbeu ya Aroni, asasendere kucita cofukiza pamaso pa Yehova; angakhale monga Kora ndi khamu lace; monga Yehova adanena naye ndi dzanja la Mose.

Werengani mutu wathunthu Numeri 16

Onani Numeri 16:40 nkhani