Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Numeri 10:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo tsiku lakukondwera inu, ndi nyengo zoikidwa zanu, ndi poyamba miyezi yanu, muziliza malipenga pa nsembe zanu zopsereza, ndi pa nsembe zanu zoyamika; ndipo akhale kwa inu cikumbutso pamaso pa Mulungu wanu; Ine ndine Yehova Mulungu wanu.

Werengani mutu wathunthu Numeri 10

Onani Numeri 10:10 nkhani