Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati Alevi, Yesuwa, ndi Kadimiyeli, Buni, Hasabineya, Serebiya, Hodiya, Sebaniya, ndi Petatiya, Imirirani, lemekezani Yehova Mulungu wanu ku nthawi za nthawi; ndipo lilemekezeke dzina lanu la ulemerero, lokuzika loposa cilemekezo ndi ciyamiko conse.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:5 nkhani