Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:28 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma atapumula, anabwereza kucita coipa pamaso panu; cifukwa cace munawasiya m'dzanja la adani ao amene anacita ufumu pa iwo; koma pobwera iwo ndi kupfuula kwa Inu, munamva m'Mwamba ndi kuwapulumutsa kawiri kawiri, monga mwa cifundo canu;

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:28 nkhani