Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndipo munawacitira umboni, kuti muwabwezerenso ku cilamulo canu; koma anacita modzikuza, osamvera malamulo anu; koma anacimwira malamulo anu (amene munthu akawacita adzakhala nao ndi moyo); nakaniza phewa lao, naumitsa khosi lao, osamvera.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:29 nkhani