Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 9:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cifukwa cace munawapereka m'dzanja la adani ao akuwasautsa; koma mu nthawi ya kusautsika kwao anapfuula kwa Inu, ndipo munamva m'Mwamba, ndi monga mwa nsoni zanu zambiri munawapatsa apulumutsi akuwapulumutsa m'dzanja la adani ao.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 9

Onani Nehemiya 9:27 nkhani