Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 8:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Naturuka anthu, nakazitenga, nadzimangira misasa, yense pa tsindwi la nyumba yace, ndi m'mabwalo ao, ndi m'mabwalo a nyumba ya Mulungu, ndi pa khwalala la cipata ca kumadzi, ndi pa khwalala la cipata ca Efraimu.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 8

Onani Nehemiya 8:16 nkhani