Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinakutumulanso maraya anga, ndi kuti, Mulungu akutumule momwemo munthu yense wosasunga mau awa, ku nyumba yace, ndi ku nchito yace; inde amkutumule momwemo, namtayire zace zonse. Ndi msonkhano wonse unati, Amen, nalemekeza Yehova. Ndipo anthu anacita monga mwa mau awa.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 5

Onani Nehemiya 5:13 nkhani