Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 5:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anati, Tidzawabwezera osawalipitsa kanthu, tidzacita monga momwe mwanena. Pamenepo ndinaitana ansembe, ndi kuwalumbiritsa, kuti adzacita monga mwa mau awa.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 5

Onani Nehemiya 5:12 nkhani