Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Nehemiya 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potsatizana naye anakonza Nehemiya mwana wa Azibuki, mkuru wa dera lace lina la dziko la Bete Zuri, mpaka malo a pandunji pa manda a Davide, ndi ku dziwe adalikumba, ndi ku nyumba ya amphamvu aja.

Werengani mutu wathunthu Nehemiya 3

Onani Nehemiya 3:16 nkhani