Koma adzakhala munthu yense patsinde pa mpesa wace, ndi patsinde pa mkuyu wace; ndipo sipadzakhala wakuwaopsa; pakuti pakamwa pa Yehova wa makamu padanena.