Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 64:3-5 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

3. Amene anola lilime lao ngati lupanga,Napiringidza mibvi yao, ndiyo mau akuwawitsa;

4. Kuponyera wangwiro mobisika:Amponyera modzidzimutsa, osaopa.

5. Alimbikitsana m'cinthu coipa;Apangana za kuchera misampha mobisika;Akuti, Adzaiona ndani?

Werengani mutu wathunthu Masalmo 64