Afunafuna zosalungama; kusanthula, asanthuladi kutha;Cingakhale ca m'kati mwace mwa munthu, ndi mtima wozama.