Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 53:5-6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

5. Pamenepo anaopa kwakukuru, popanda cifukwa ca kuopa:Pakuti Mulungu anamwaza mafupa a iwo akuzinga iwe;Unawacititsa manyazi, pakuti Mulungu anawakaniza.

6. Ha, cipulumutso ca Israyeli cicokere m'Ziyoni!Pakubweretsa Mulungu anthu ace a m'ndende,Yakobo adzakondwera, Israyeli adzasekera.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 53