Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 51:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Mundicitire ine cifundo, Mulungu,Monga mwa kukoma mtima kwanu;Monga mwa unyinji wa nsoni zokoma zanuMufafanize macimo anga.

2. Mubwereze kunditsuka mphulupulu yanga,Ndipo mundiyeretse kundicotsera coipa canga,

3. Cifukwa ndazindikira macimo anga;Ndipo coipa canga ciri pamaso panga cikhalire:

Werengani mutu wathunthu Masalmo 51