Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 51:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pa Inu, Inu nokha, ndinacimwa,Ndipo ndinacicita coipaco pamaso panu:Kuti mukhale wolungama pakulankhula Inu,Mukhalenso woyera pa kuweruza kwanu.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 51

Onani Masalmo 51:4 nkhani