Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 40:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Cilungamo canu sindinacibisa m'kati mwamtima mwanga;Cikhulupiriko canu ndi cipulumutso canu ndinacinena;Cifundo canu ndi coonadi canu sindinacibisira msonkhano waukuru.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 40

Onani Masalmo 40:10 nkhani