Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

Masalmo 39:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndinati, Ndidzasunga njira zanga,Kuti ndingacimwe ndi lilime langa:Ndidzasunga pakamwa panga ndi cam'kamwa,Pokhala woipa ali pamaso panga.

Werengani mutu wathunthu Masalmo 39

Onani Masalmo 39:1 nkhani